Yophunzila
JULY 2021
NKHANI ZOPHUNZILA: AUGUST 30–SEPTEMBER 26, 2021
© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa donate.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
CITHUNZI CA PACIKUTO:
Ophunzila a Yesu anali kum’konda cifukwa sanali kudziona kukhala woposa iwo. Anali kukonda kuceza na mabwenzi ake (Onani nkhani yophunzila 29, ndime 12)