Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
MMENE ZOPELEKA ZANU ZIMAGWILILA NCHITO
Kodi nchito yathu imacilikizidwa bwanji ku maiko amene ni osauka?
Pitani pa jw.org ku Cizungu, pa mbali yakuti LIBRARY > ARTICLE SERIES > HOW YOUR DONATIONS ARE USED.
ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA
Kodi Ndingatani Kuti Maganizo Anga Azikhala pa Zimene Ndikupanga?
Onani mbali zitatu zimene zipangizo zamakono, zingapangitse kuti musaike maganizo anu pa cinthu cimodzi, komanso zimene mungacite kuti muzikwanitsa kuika maganizo anu pa cinthu cimodzi.
Pitani pa jw.org ku Chichewa, pa mbali yakuti LAIBULALE > NKHANI ZOSIYANASIYANA > ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA.