Yophunzila
OCTOBER 2021
NKHANI ZOPHUNZILA: DECEMBER 6, 2021–JANUARY 2, 2022
© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa donate.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
CITHUNZI CA PACIKUTO
Olo kuti Nowa analalikila mokhulupilika kwa zaka zambili, palibe anapulumuka kupatulapo iye na banja lake. Ngakhale n’telo, iye anakhalabe womvela kwa Mulungu! (Onani nkhani yophunzila 43, ndime 11)