Yophunzila
NOVEMBER 2022
NKHANI ZOPHUNZILA: JANUARY 2-29, 2023
© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa donate.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
CITHUNZI CA PACIKUTO:
Ezekieli akuona masomphenya a galeta la Yehova. Ndipo masomphenyawo akum’patsa cidalilo cakuti Yehova adzam’thandiza kucita utumiki wake (Onani nkhani yophunzila 45, ndime 7)