Zamkatimu
ZA M’KOPE INO
Nkhani Yophunzila 45: January 2-8, 2023
2 Mmene Yehova Amatithandizila Kugwila Nchito Yolalikila
Nkhani Yophunzila 46: January 9-15, 2023
8 Kodi Yehova Amatithandiza Bwanji Kupilila Mwacimwemwe?
Nkhani Yophunzila 47: January 16-22, 2023
14 Musalole Ciliconse Kukulekanitsani na Yehova
Nkhani Yophunzila 48: January 23-29, 2023
20 Khalanibe Oganiza Bwino Kukhulupilika Kwanu Kukayesedwa
26 Mbili Yanga—“N’nakwanilitsa Colinga Canga Cotumikila Yehova”