Zina Zimene Zilipo Pa JW.ORG
MMENE ZOPELEKA ZANU ZIMAGWILILA NCHITO
Laibulali Imene Mungathe Kuinyamula Kumanja
Ŵelengani kuti mudziŵe zimene zimafunika kuti JW Laibulali izigwila bwino nchito.
MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA
Muziona Moyenera Zinthu Zimene Zimakukwiyitsani
M’malo molola zinthu zimene zimakukwiyitsani kuyambitsa mikangano pakati pa inu na mnzanu wa mu ukwati, phunzilani kuona zinthuzo moyenela.
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
“Misewu Ndi Imene Inali Nyumba Yanga”
Antonio anali waciwawa, anali kugwilitsa nchito mankhwala osokoneza ubongo, komanso kumwa moŵa mwaucidakwa. Izi zinam’pangitsa kuona kuti moyo ulibe phindu. N’ciyani cinam’thandiza kusintha umoyo wake?