LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • g18 na. 1 tsa. 16
  • Dziŵani Zambili

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Dziŵani Zambili
  • Galamuka!—2018
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • KODI MUNADZIFUNSAPO KUTI:
  • MUNGAPEZE MAYANKHO PA MAFUNSO AMENEWA NA ENA
  • Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambili Onena za Umoyo?
    Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambili Onena za Umoyo?
  • Kodi Munadzifunsapo?
    Galamuka!—2019
  • Mfundo Yothandiza Pa Kuŵelenga Kwanu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Kabokosi Kakang’ono Kopelekela Cakudya Cauzimu
    Mmene Zopeleka Zanu Zimagwilila Nchito
Onaninso Zina
Galamuka!—2018
g18 na. 1 tsa. 16
Kupeza mayankho pa webusaiti ya jw.org

NJILA YOPEZELA CIMWEMWE

Dziŵani Zambili

KODI MUNADZIFUNSAPO KUTI:

  • Ningacite ciani kuti banja langa likhale lacimwemwe?

  • Ningacite ciani kuti nipeze mabwenzi abwino na kukhala bwenzi labwino?

  • Kodi pali ciyembekezo canji cokhudza okondedwa anga amene anamwalila?

  • Kodi mavuto adzathadi?

  • Kodi anthu adzafika poliwonongelatu dziko lapansi?

  • Kodi zipembedzo zonse zimatsogolela anthu kwa Mulungu woona?

MUNGAPEZE MAYANKHO PA MAFUNSO AMENEWA NA ENA

Yendani pa webusaiti ya jw.org, imene ipezeka m’vitundu voposa 900. Pamenepo mudzapeza mfundo zothandiza pa nkhani zosiyana-siyana.

Mudzakondwela kutamba mavidiyo okamba za anthu azikhalidwe zosiyana-siyana amene apeza njila yopezela cimwemwe, ndipo ali na umoyo wacimwemwe. Ena anali kuseŵenzetsa amkola bongo, ena anali akaidi. Enanso ni ophunzila kwambili, ndipo ena ni asayansi.

Pa jw.org mungaŵelenge kapena kucita daunilodi Baibo na mabuku ena osiyana-siyana mahala. Mudzapezapo mabuku ambili kuphatikizapo otsatilawa:

  • N’zotheka Banja Lanu Kukhala Lacimwemwe

  • Njila ya Kumoyo Wamuyaya—Kodi Mwaipeza?

  • Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani