LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • g19 na. 1 tsa. 16
  • Kodi Munadzifunsapo?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Munadzifunsapo?
  • Galamuka!—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Seŵenzetsani Tsamba Loyamba la JW.ORG mu Ulaliki
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Mmene Tingagwilitsile Nchito Zinthu Zongomvetsela za pa jw.org
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Dziŵani Zambili
    Galamuka!—2018
  • Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambili Onena za Umoyo?
    Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambili Onena za Umoyo?
Onaninso Zina
Galamuka!—2019
g19 na. 1 tsa. 16

Kodi Munadzifunsapo?

Atate na mwana akuyang’ana pa webusaiti ya jw.org
  • Ngati Mulungu amasamala za ise, n’cifukwa ciani walola zoipa na mavuto kupitiliza kukhalapo kwa nthawi yaitali?

  • Kodi tingatsimikize bwanji kuti tili m’masiku otsiliza a dzikoli?

  • Kodi tingadziŵe bwanji kuti malonjezo a m’Baibo okamba za Ufumu wa Mulungu adzakwanilitsidwa?

  • Kodi Baibo ingatithandize kupanga zosankha zanzelu mu umoyo wathu palipano?

Cifukwa cakuti Mlengi wathu amatikonda, iye wapeleka mayankho pa mafunso amenewa na ena ambili. Pokuthandizani kupeza mayankho, yendani pa webusaiti yathu ya www.jw.org, imene colinga cake ni kuthandiza anthu kudziŵa bwino Baibo.

Pa webusaiti imeneyi, mungapezepo zimene ise Mboni za Yehova timacita, nkhani zosiyana-siyana, mavidiyo, zomvetsela, kufunsa anthu mafunso, komanso mabuku ena ambili kuphatikizapo Baibo. Zonse ni mahala, ndipo simukakamizidwa kukhala wa Mboni.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani