LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • g21 na. 1 tsa. 3
  • Nzelu Zokuthandizani Kukhala na Umoyo Wacimwemwe

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Nzelu Zokuthandizani Kukhala na Umoyo Wacimwemwe
  • Galamuka!—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Zamkatimu
    Galamuka!—2021
  • Nzelu Yeniyeni Imafuula
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2022
  • Mmene Mungaipezele
    Galamuka!—2018
Galamuka!—2021
g21 na. 1 tsa. 3
Mayi ali pamalo odyela a m’mbali mwa njila ku India, ndipo akusinkhasinkha zimene waŵelenga.

Nzelu Zokuthandizani Kukhala na Umoyo Wacimwemwe

“Nimamva cisoni nikaona zoipa zimene zimacitika padzikoli, monga nkhondo, umphawi, matenda, na kuzunzidwa kwa ana. Ngakhale n’conco, nili na ciyembekezo.”—RANI.a

Rani anapeza cimwemwe ceniceni ataphunzila za Mlengi wathu, Mulungu wamphamvuzonse, amene ni Gwelo la nzelu zenizeni. Pamene muŵelenga nkhani zotsatilazi, onani mmene ziphunzitso zake zingakuthandizileni . . .

  • kukhala na banja lacimwemwe

  • kukhala mwamtendele na anthu ena

  • kukhala wokhutila

  • kudziŵa cifukwa cake timavutika komanso kufa

  • kukhala na ciyembekezo codalilika ca tsogolo labwino

  • kum’dziŵa bwino Mlengi wathu na kukhala naye paubwenzi

Mudzaonanso kuti Mlengi wathu amapeleka nzelu kwa aliyense amene amazifuna-funa, osati kwa anthu oŵelengeka cabe.

a Maina m’magazini ino asinthidwa.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani