LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 63
  • Tikhale Okhulupirika Nthawi Zonse

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tikhale Okhulupirika Nthawi Zonse
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Tikhale Okhulupilika Nthawi Zonse
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Kodi Cikondi Cosasintha ca Yehova N’ciani?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • Cikondi Cokhulupilika Cimam’kondweletsa Yehova—Nanga Imwe?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Tengelani Citsanzo ca Atumiki Okhulupilika a Yehova
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 63

Nyimbo 63

Tikhale Okhulupirika Nthawi Zonse

(Salimo 18:25)

1. Tikhulupirike zedi

Kwa M’lungu ndi kum’konda.

Kuphunzira malamulo

Ake tifunikira.

Sangatigwiritse mwala

Tikamamvera Iye.

Ndi wokhulupirikadi

Ndipo sitingam’siye.

2. Tikhulupirike zedi

Kwa ’bale pamavuto,

Tikhale okoma mtima

M’mawu ndiponso m’ntchito.

Tilemekeze abale,

Tiwakhulupirire.

Baibulo litigwirizanitse

Nthawi zonse.

3. Tikhulupirike zedi

Tikamalangizidwa,

Ndi abale amumpingo,

Tifunika kumvera.

Tidzapeza madalitso

Ochoka kwa Yehova.

Tikakhulupirikadi

Iye adzatikonda.

(Onaninso Sal. 149:1; 1 Tim. 2:8; Aheb. 13:17.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani