LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 131
  • Yehova Amapereka Chipulumutso

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Amapereka Chipulumutso
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Amapulumutsa
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nilimbitseni Mtima
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Cuma Capadela
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Cuma Capadela
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 131

Nyimbo 131

Yehova Amapereka Chipulumutso

(2 Samueli 22:1-8)

1. Yehova ndinu M’lungu wamphamvuyonse.

Timaona izi m’chilengedwe chonse.

Kulibe m’lungu wina angachite zimene

Inu mumachita.

(KOLASI)

Yehova amapatsa pothawira.

Tidzaonadi kuti iye ndi Thanthwe.

Choterotu tilengezebe za Yehova

Mpulumutsi wathu. Titero mosaopa.

2. Ngakhale zingwe za imfa zandizinga

Ndikupempha kuti ndilimbedi mtima.

Mumve pemphero langa: “Nditetezeni chonde,

Ndipulumutseni.”

(KOLASI)

Yehova amapatsa pothawira.

Tidzaonadi kuti iye ndi Thanthwe.

Choterotu tilengezebe za Yehova

Mpulumutsi wathu. Titero mosaopa.

3. Mawu anu onga bingu adzamveka.

Olimbana nanu adzanjenjemera.

Mudzakhala chimene mukufuna kukhala.

Onse adzaona.

(KOLASI)

Yehova amapatsa pothawira.

Tidzaonadi kuti iye ndi Thanthwe.

Choterotu tilengezebe za Yehova

Mpulumutsi wathu. Titero mosaopa.

(Onaninso Sal. 18:1, 2; 144:1, 2.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani