LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • ll gao 2 masa. 6-7
  • Kodi Mulungu Woona Ndani?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mulungu Woona Ndani?
  • Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
  • Nkhani Zofanana
  • Gao 2
    Mvetselani kwa Mulungu
  • Kodi Mulungu N’ndani?
    Zimene Baibulo Ingatiphunzitse
  • Kucokela pa Cilengedwe Kufika pa Cigumula
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Zimene Baibo Imatiuza
    Galamuka!—2021
Onaninso Zina
Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
ll gao 2 masa. 6-7

GAO 2

Kodi Mulungu Woona Ndani?

Ali pa mpando wake wacifumu kumwamba, Yehova akuyang’ana zimene analenga, za kumwamba ndi za padziko lapansi

Pali Mulungu woona mmodzi cabe, ndipo dzina lake ni Yehova. (Salimo 83:18) Iye ni Mzimu, sitingamuone. Amatikonda ndipo amafuna kuti ife tizimukonda. Amafunanso kuti tizikonda anthu anzathu. (Mateyu 22:35-40) Iye ni Wamphamvuyonse, ni Mlengi wa zinthu zonse.

Pa zolengedwa zake zonse, Mulungu anayambilila kulenga mngelo mmodzi wamphamvu. Mngelo ameneyo ndiye anabwela kukhala Yesu Kristu. Pambuyo pake Yehova analenga angelo ena.

Yehova analenga zinthu zonse za kumwamba . . . ndi za padziko lapansi. Chivumbulutso 4:11

Yehova analenga nyenyezi, dziko lapansi, ndi zonse za padziko.—Genesis 1:1.

Anaumba Adamu, munthu woyamba, ndi dothi lapansi.—Genesis 2:7.

  • N’cifukwa ciani tiyenela kulemekeza Yehova?—Yesaya 42:5.

  • Kodi makhalidwe ena a Mulungu ndi ati?—Ekisodo 34:6.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani