Phunzilo 5
1 Atesalonika 5:18
Ngati mnzako akupatsa mphatso kapena ngati akucitila cinthu cabwino, uyenela kumwetulila kwambili
Kulikonse kumene ungakhale komanso pamene ucita ciliconse, Nthawi Zonse uzikumbukila kukamba “Zikomo!”
ZOCITA
Muŵelengeleni mwana wanu:
1 Atesalonika 5:18
Uzani mwana wanu kuti aloze:
Mphatso Mnyamata
Citseko Cakudya
Pezani zinthu zobisika.
Apulo Telefoni
M’funseni mwana wanu:
N’cifukwa ciani n’cinthu cabwino kukamba “Zikomo”?
[Cithunzi 12]
[Cithunzi 13]
[Cithunzi 13]
[Cithunzi 13]