LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • snnw nyimbo 136 tsa. 1
  • Ufumu Ulamulila—Ubwele!

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ufumu Ulamulila—Ubwele!
  • Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Nkhani Zofanana
  • Ufumu Ulamulila—Ubwele!
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Yehova Ndiye Mfumu Yathu!
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Yehova ndi Mfumu Yathu
    Imbirani Yehova
  • Munapeleka Mwana Wanu Wobadwa Yekha
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
Onaninso Zina
Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
snnw nyimbo 136 tsa. 1

Nyimbo 136

Ufumu Ulamulila—Ubwele!

Yopulinta

(Chivumbulutso 11:15; 12:10)

  1. Yehova Mulungu wathu,

    Ndimwe wamuyaya.

    Mwalonga Yesu Ufumu;

    Mwa kufuna kwanu.

    Khristu akulamulila;

    Adzalamulila konse.

    (KOLASI)

    Lomba zafikadi

    Cipulumutso, na mphamvu.

    Ufumu wabadwa.

    Timapemphela: “Ubwele!”

  2. Satana ‘dzaonongedwa

    Kwatsala pang’ono.

    Ise tingasautsike

    Koma timadziŵa:

    Khristu akulamulila;

    Adzalamulila konse.

    (KOLASI)

    Lomba zafikadi

    Cipulumutso, na mphamvu.

    Ufumu wabadwa.

    Timapemphela: “Ubwele!”

  3. Angelo asekelela

    Aimba mokondwa.

    Satana n’ziwanda zake

    Anagonjetsewa.

    Khristu akulamulila;

    Adzalamulila konse.

    (KOLASI)

    Lomba zafikadi

    Cipulumutso, na mphamvu.

    Ufumu wabadwa.

    Timapemphela: “Ubwele!”

(Onaninso Dan. 2:34, 35; 2 Akor. 4:18.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani