LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 9
  • Yehova Ndiye Mfumu Yathu!

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Ndiye Mfumu Yathu!
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova ndi Mfumu Yathu
    Imbirani Yehova
  • Ufumu Ulamulila—Ubwele!
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Ufumu Ulamulila—Ubwele!
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • “Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka”
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 9

NYIMBO 9

Yehova Ndiye Mfumu Yathu!

Yopulinta

(Salimo 97:1)

  1. 1. Kondwa, lemekeza Yehova,

    Cifukwa iye ni wacilungamo.

    Timuyimbile nyimbo zacitamando;

    Onse adziŵe nchito zake.

    (KOLASI)

    Miyamba ikondwe, Dziko likondwele,

    Cifukwa Yehova ni Mfumu!

    Miyamba ikondwe, Dziko likondwele,

    Cifukwa Yehova ni Mfumu!

  2. 2. Tidziŵitse mitundu yonse;

    Kuti Mulungu amapulumutsa.

    Yehova ni Mfumu; onse am’tamande.

    Tiyeni’fe timulambile.

    (KOLASI)

    Miyamba ikondwe, Dziko likondwele,

    Cifukwa Yehova ni Mfumu!

    Miyamba ikondwe, Dziko likondwele,

    Cifukwa Yehova ni Mfumu!

  3. 3. Ufumu wakhazikitsidwa.

    Ndipo Yesu Khristu lomba ni Mfumu.

    Milungu ya dziko icite manyazi;

    Tidzamutamanda Yehova.

    (KOLASI)

    Miyamba ikondwe, Dziko likondwele,

    Cifukwa Yehova ni Mfumu!

    Miyamba ikondwe, Dziko likondwele,

    Cifukwa Yehova ni Mfumu!

(Onaninso 1 Mbiri 16:9; Sal. 68:20; 97:6, 7.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani