LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 35
  • ‘Tsimikizilani Zinthu Zofunika Kwambili’

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • ‘Tsimikizilani Zinthu Zofunika Kwambili’
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • “Muzitsimikizira Kuti Zinthu Zofunika Kwambiri Ndi Ziti”
    Imbirani Yehova
  • Uziyenda na Mulungu
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Kodi Mumamvela Bwanji?
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Kodi Mumamvela Bwanji?
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 35

NYIMBO 35

‘Tsimikizilani Zinthu Zofunika Kwambili’

Yopulinta

(Afilipi 1:10)

  1. 1. Lomba ndiye nthawi yakuti tikhale

    Ozindikila.

    Inde, zinthu zoona ndi zofunika

    Kuti ticite.

    (KOLASI)

    Ukadziŵa na kucita,

    Zofunika;

    Udzamusangalatsa Yehova.

    Udzapeza,

    Madalitso osaneneka!

  2. 2. Conco tonse tilalikile uthenga

    Kwa anthu onse.

    Kuthandiza a njala ya coonadi

    Kudziŵa M’lungu.

    (KOLASI)

    Ukadziŵa na kucita,

    Zofunika;

    Udzamusangalatsa Yehova.

    Udzapeza,

    Madalitso osaneneka!

  3. 3. Tikacita zofunika tidzakhala,

    Osangalala.

    Tidzakhala na mtendele woculuka

    Moyo wabwino.

    (KOLASI)

    Ukadziŵa na kucita,

    Zofunika;

    Udzamusangalatsa Yehova.

    Udzapeza,

    Madalitso osaneneka!

(Onaninso Sal. 97:10; Yoh. 21:15-17; Afil. 4:7.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani