“Musaleme pa Kukwanilitsa Cilamulo ca Khristu!”
KUM’MAWA
8:40 Nyimbo Zamalimba
8:50 Nyimbo Na. 17 na Pemphelo
9:00 Kodi Cilamulo ca Khristu N’ciani?
9:15 Kukwanilitsa Cilamulo ca Khristu Pamene Ena Sakutiona
9:30 Kukwanilitsa Cilamulo ca Khristu mu Ulaliki
9:55 Nyimbo Na. 70 na Zilengezo
10:05 Cilamulo ca Khristu—N’cifukwa Ciani N’copambana?
10:35 Kudzipeleka na Ubatizo
11:05 Nyimbo Na. 51
KUMASANA
12:20 Nyimbo Zamalimba
12:30 Nyimbo Na. 76
12:35 Zocitika mu Ulaliki
12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:15 Kukwanilitsa Cilamulo ca Khristu M’banja
13:30 Kukwanilitsa Cilamulo ca Khristu ku Sukulu
13:45 Nyimbo Na. 35 na Zilengezo
13:55 Tizikondana Wina na Mnzake, Mmene Yesu Anatikondela
14:55 Nyimbo Na. 13 na Zilengezo