Pezani Mayankho pa Mafunso Aya:
Kodi “cilamulo ca Khristu” n’ciani? (Agal. 6:2)
Kodi tingakwanilitse bwanji cilamulo ca Khristu pamene ena sakutiona? (1 Akor. 10:31)
Kodi timakwanilitsa bwanji cilamulo ca Khristu mu ulaliki? (Luka 16:10; Mat. 22:39; Mac. 20:35)
Kodi cilamulo ca Khristu cimapambana bwanji Cilamulo ca Mose? (1 Pet. 2:16)
Kodi okwatilana ndi makolo angakwanilitse bwanji cilamulo ca Khristu m’banja lawo? (Aef. 5:22, 23, 25; Aheb. 5:13, 14)
Kodi mungakwanilitse bwanji cilamulo ca Khristu ku sukulu? (Sal. 1:1-3; Yoh. 17:14)
Kodi tingawakonde bwanji anthu ena mmene Yesu anakondela ife? (Agal. 6:1-5, 10)