LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • CO-pgm21 tsa. 8
  • Mawu kwa Osonkhana

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mawu kwa Osonkhana
  • Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2021
  • Nkhani Zofanana
  • Mawu kwa Osonkhana
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2022
  • Mawu kwa Osonkhana
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2020
  • Mawu kwa Osonkhana
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2023
  • Mawu kwa Osonkhana
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2024
Onaninso Zina
Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2021
CO-pgm21 tsa. 8

Mawu kwa Osonkhana

UBATIZO Akulu a mpingo wanu anapanga makonzedwe a mmene ubatizo wanu udzacitikila pambuyo pa cigawo ca m’maŵa pa Tsiku Laciŵili.

ZOPELEKA Msonkhano uno ukumasulidwa m’zinenelo zoposa 400. Zopeleka zanu zaufulu zimathandiza pa nchito ya padziko lonse imeneyi. Mungacite copeleka kupitila pa intaneti mwa kupita pa copeleka.jw.org. Timayamikila kwambili zopeleka zanu zonse. Bungwe Lolamulila limayamikila ngako kuwolowa manja kwanu kocilikiza zinthu za Ufumu.

Alongo aŵili aimilila pafupi na kasitandi kaulaliki, ndipo akulalikila munthu mu msewu ku India.

SUKULU YA ALENGEZI A UFUMU Apainiya a zaka 23 mpaka 65, amene afuna kuwonjezela utumiki wawo, akupemphedwa kuonana na kalembela wa mpingo wawo kuti asaine fomu ya pa intaneti, yofunsila kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu.

Wokonzedwa na Bungwe Lolamulila la Mboni za Yehova

© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani