Tsiku Lacitatu
‘Ngati muli ndi cikhulupililo . . . , zidzacitikadi’—Mateyu 21:21
M’MAŴA
9:20 Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 137 na Pemphelo
9:40 YOSIYILANA: Tengelani Citsanzo ca Akazi a Cikhulupililo Colimba!
• Sara (Aheberi 11:11, 12)
• Rahabi (Aheberi 11:31)
• Hana (1 Samueli 1:10, 11)
• Kamtsikana Kaciisiraeli Kotengeledwa ku Ukapolo (2 Mafumu 5:1-3)
• Mariya Mayi wa Yesu (Luka 1:28-33, 38)
• Mayi wa ku Foinike (Mateyu 15:28)
• Marita (Yohane 11:21-24)
• Zitsanzo Zamakono (Salimo 37:25; 119:97, 98)
11:05 Nyimbo Na. 142 na Zilengezo
11:15 NKHANI YA ANTHU ONSE: “Khulupililani Uthenga Wabwino” (Maliko 1:14, 15; Mateyu 9:35; Luka 8:1)
11:45 Nyimbo Na. 22 na Kupumula
MASANA
13:35 Vidiyo ya Nyimbo
13:45 Nyimbo Na. 126
13:50 SEŴELO LA M’BAIBO: Danieli: Citsanzo Cokhala Wokhulupilika kwa Moyo Wonse— Gawo 2 (Danieli 5:1–6:28; 10:1–12:13)
14:40 Nyimbo Na. 150 na Zilengezo
14:45 Khalani Amphamvu mwa Cikhulupililo Canu! (Danieli 10:18, 19; Aroma 4:18-21)
15:45 Nyimbo Yatsopano na Pemphelo Lothela