Tsiku Lacitatu
“Amene adzapilile mpaka pa mapeto, ndiye amene adzapulumuke”—MATEYU 24:13
KUM’MAŴA
- 8:20 Nyimbo za Pavidiyo 
- 8:30 Nyimbo 83 na Pemphelo 
- 8:40 YOSIILANA: Tifunika ‘Kuthamanga Mopilila’ - Thamangani Kuti Mupambane! (1 Akorinto 9:24) 
- Konzekelani Mwakhama (1 Akorinto 9:25-27) 
- Tayani Zolemetsa Zosafunika (Aheberi 12:1) 
- Tengelani Zitsanzo Zabwino (Aheberi 12:2, 3) 
- Idyani Zakudya Zopatsa Thanzi (Aheberi 5:12-14) 
- Imwani Madzi Ambili (Chivumbulutso 22:17) 
- Tsatilani Malamulo a Mpikisano (2 Timoteyo 2:5) 
- Khalani na Cidalilo Cakuti Mudzalandila Mphoto (Aroma 15:13) 
 
- 10:10 Nyimbo 130 na Zilengezo 
- 10:20 NKHANI YA ANTHU ONSE: Musataye Mtima! (Yesaya 48:17; Yeremiya 29:11) 
- 10:50 Cidule ca Nsanja ya Mlonda 
- 11:20 Nyimbo 148 na Kupumula 
KUMASANA
- 12:35 Nyimbo za Pavidiyo 
- 12:45 Nyimbo 142 
- 12:50 SEŴELO: “Kumbukilani Mkazi wa Loti”—Mbali 3(Luka 17:28-33) 
- 13:20 Nyimbo 65 na Zilengezo 
- 13:30 “Uziwayembekezelabe . . . Iwo Sadzacedwa!”(Habakuku 2:3) 
- 14:30 Nyimbo 154 na Pemphelo Lothela