Tsiku Lacitatu
“Mulungu amene amapeleka ciyembekezo akudzazeni ndi cimwemwe conse”—Aroma 15:13
M’maŵa
- 8:20 Vidiyo ya Nyimbo 
- 8:30 Nyimbo Na. 101 na Pemphelo 
- 8:40 YOSIYILANA: Anafesa Mtendele na Kututanso Mtendele - • Yosefe na Abale Ake (Agalatiya 6:7, 8; Aefeso 4:32) 
- • Agibeoni (Aefeso 5:17) 
- • Gidiyoni (Oweruza 8:2, 3) 
- • Abigayeli (1 Samueli 25:27-31) 
- • Mefiboseti (2 Samueli 19:25-28) 
- • Paulo na Baranaba (Machitidwe 15:36-39) 
- • Zitsanzo Zamakono (1 Petulo 2:17) 
 
- 10:05 Nyimbo Na. 28 na Zilengezo 
- 10:15 NKHANI YA ANTHU ONSE: N’zotheka Kukhala Paubwenzi na Mulungu—Motani? (Yakobo 4:8; 1 Yohane 4:10) 
- 10:45 Nyimbo Na. 147 na Kupumula 
Masana
- 12:35 Vidiyo ya Nyimbo 
- 12:45 Nyimbo Na. 23 
- 12:50 SEŴELO LA M’BAIBO: Yehova Akutitsogolela Panjila ya Mtendele—Gawo 2 (Yesaya 48:17, 18) 
- 13:30 Nyimbo Na. 139 na Zilengezo 
- 13:40 Mtendele wa Cilengedwe Conse Udzabwela Ndithu! (Aroma 16:20; 1 Akorinto 15:24-28; 1 Yohane 3:8) 
- 14:40 Nyimbo Yatsopano na Pemphelo Lothela