Tsiku Lacitatu
‘Ngati muli ndi cikhulupililo . . . , zidzacitikadi’—Mateyu 21:21
M’MAŴA
- 9:20 Vidiyo ya Nyimbo 
- 9:30 Nyimbo Na. 137 na Pemphelo 
- 9:40 YOSIYILANA: Tengelani Citsanzo ca Akazi a Cikhulupililo Colimba! - • Sara (Aheberi 11:11, 12) 
- • Rahabi (Aheberi 11:31) 
- • Hana (1 Samueli 1:10, 11) 
- • Kamtsikana Kaciisiraeli Kotengeledwa ku Ukapolo (2 Mafumu 5:1-3) 
- • Mariya Mayi wa Yesu (Luka 1:28-33, 38) 
- • Mayi wa ku Foinike (Mateyu 15:28) 
- • Marita (Yohane 11:21-24) 
- • Zitsanzo Zamakono (Salimo 37:25; 119:97, 98) 
 
- 11:05 Nyimbo Na. 142 na Zilengezo 
- 11:15 NKHANI YA ANTHU ONSE: “Khulupililani Uthenga Wabwino” (Maliko 1:14, 15; Mateyu 9:35; Luka 8:1) 
- 11:45 Nyimbo Na. 22 na Kupumula 
MASANA
- 13:35 Vidiyo ya Nyimbo 
- 13:45 Nyimbo Na. 126 
- 13:50 SEŴELO LA M’BAIBO: Danieli: Citsanzo Cokhala Wokhulupilika kwa Moyo Wonse— Gawo 2 (Danieli 5:1–6:28; 10:1–12:13) 
- 14:40 Nyimbo Na. 150 na Zilengezo 
- 14:45 Khalani Amphamvu mwa Cikhulupililo Canu! (Danieli 10:18, 19; Aroma 4:18-21) 
- 15:45 Nyimbo Yatsopano na Pemphelo Lothela