NYIMBO 147
Lonjezo la Moyo Wamuyaya
Yopulinta
	(Salimo 37:29)
- 1. Mulungu watilonjeza, - Moyo wokondweletsa. - Ngati ticita zabwino, - Tidzaulandila. - (KOLASI) - Moyo wamuyaya, - M’lungu walonjeza, - Iye sanganame, - Zidzacitika. 
- 2. Ana onse a Yehova, - Adzakhala angwilo. - Mu Ufumu wa Mulungu, - Tidzasangalala. - (KOLASI) - Moyo wamuyaya, - M’lungu walonjeza, - Iye sanganame, - Zidzacitika. 
- 3. Posacedwa’pa Mulungu, - Adzaukitsa anthu. - Mitundu yonse ya anthu, - Idzadalitsika. - (KOLASI) - Moyo wamuyaya, - M’lungu walonjeza, - Iye sanganame, - Zidzacitika. 
(Onaninso Yes. 25:8; Luka 23:43; Yoh. 11:25; Chiv. 21:4.)