LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • CO-pgm20 masa. 6-7
  • Tsiku Lacitatu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tsiku Lacitatu
  • Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2020
  • Nkhani Zofanana
  • Tsiku Lacitatu
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2024
  • Tsiku Lacitatu
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2017
  • Tsiku Lacitatu
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2023
  • Tsiku Loyamba
    Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2024
Onaninso Zina
Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2020
CO-pgm20 masa. 6-7
Zithunzi: 1. Okwatilana okalamba ali m’motoka yawo. Mwacimwemwe, apeleka moni kwa munthu amene akudutsa. 2. Banja la m’nthawi za m’Baibo laimilila m’bwalo la kacisi ku Yerusalemu.

TSIKU LACITATU

“Sangalala mwa Yehova, ndipo adzakupatsa zokhumba za mtima wako”​—Salimo 37:4

KUM’MAŴA

  • 8:20 Vidiyo ya Nyimbo

  • 8:30 Nyimbo Na. 22 na Pemphelo

  • 8:40 YOSIILANA: Tingakhalebe Okondwela Ngakhale . . .

    • • pa Masautso (Aroma 5:3-5; 8:35, 37)

    • • pa Zowawa (2 Akorinto 4:8; 7:5)

    • • pa Mazunzo (Mateyu 5:11, 12)

    • • pa Njala (Afilipi 4:11-13)

    • • pa Usiwa (1 Akorinto 4:11, 16)

    • • pa Zoopsa (2 Akorinto 1:8-11)

    • • pa Lupanga (2 Timoteyo 4:6-8)

  • 10:10 Nyimbo Na. 9 na Zilengezo

  • 10:20 NKHANI YA ANTHU ONSE: Kondwelani na Cuma Copanda Zopweteka—Motani? (Miyambo 10:22; 1 Timoteyo 6:9, 10; Chivumbulutso 21:3-5)

  • 10:50 Cidule ca Nsanja ya Mlonda

  • 11:20 Nyimbo Na. 84 na Kupumula

KUMASANA

  • 12:40 Vidiyo ya Nyimbo

  • 12:50 Nyimbo Na. 62

  • 12:55 SEŴELO LA M’BAIBO: Nehemiya: “Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Malo Anu Acitetezo”​—Gawo 2 (Nehemiya 8:1–13:30; Malaki 1:6–3:18)

  • 13:40 Nyimbo Na. 71 na Zilengezo

  • 13:50 “Sangalala mwa Yehova”! (Salimo 16:8, 9, 11; 37:4)

  • 14:50 Nyimbo Yatsopano na Pemphelo Lothela

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani