Tsiku Loyamba
“Uthenga wabwino wa cimwemwe cacikulu cimene anthu onse adzakhale naco”—Luka 2:10
M’maŵa
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 150 na Pemphelo
8:40 NKHANI YA CHEYAMANI: N’cifukwa Ciyani Tikufunikila Uthenga Wabwino?(1 Akorinto 9:16; 1 Timoteyo 1:12)
9:10 SEŴELO LALIKULU LA M’BAIBO:
Uthenga Wabwino Wolalikidwa na Yesu: Mbali 1
Kuwala Kwenikweni kwa Dziko—Gawo Loyamba (Mateyu 1:18-25; Luka 1:1-80; Yohane 1:1-5)
9:45 Nyimbo Na. 96 na Zilengezo
9:55 YOSIYILANA: “Anatsogoleledwa na Mzimu Woyela”
• Mateyu (2 Petulo 1:21)
• Maliko (Maliko 10:21)
• Luka (Luka 1:1-4)
• Yohane (Yohane 20:31)
11:10 Nyimbo Na. 110 na Kupumula
Masana
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 117
12:50 YOSIYILANA: Khulupililani Coonadi Conena za Yesu
• Mawu (Yohane 1:1; Afilipi 2:8-11)
• Dzina Lake (Machitidwe 4:12)
• Kubadwa Kwake (Mateyu 2:1, 2, 7-12, 16)
13:30 Nyimbo Na. 99 na Zilengezo
13:40 YOSIYILANA: Zimene Tingaphunzile Tikadziŵa Bwino Kumene Yesu Anakulila
• Zacilengedwe Zopezeka ku Delalo (Deuteronomo 8:7)
• Nyama (Luka 2:8, 24)
• Zakudya (Luka 11:3; 1 Akorinto 10:31)
• Umoyo wa Panyumba (Afilipi 1:10)
• Anthu a Kudelalo (Deuteronomo 22:4)
• Maphunzilo (Deuteronomo 6:6, 7)
• Kulambila (Deuteronomo 16:15, 16)
15:15 Kodi “Uthenga Wabwino” ni Wosatha M’lingalilo Lotani? (Chivumbulutso 14:6, 7)
15:50 Nyimbo Na. 66 na Pemphelo Lothela