Tsiku Laciŵili
“Tsiku ndi tsiku muzilengeza uthenga wabwino wa cipulumutso cake”—Salimo 96:2
M’maŵa
- 8:20 Vidiyo ya Nyimbo 
- 8:30 Nyimbo Na. 53 na Pemphelo 
- 8:40 ‘Niyenela Kulengeza Uthenga Wabwino wa Ufumu’ (Luka 4:43) 
- 8:50 SEŴELO LALIKULU LA M’BAIBO: - Uthenga Wabwino Wolalikidwa na Yesu: Mbali 1 - Kuwala Kwenikweni kwa Dziko—Gawo Laciŵili (Mateyu 2:1-23; Luka 2:1-38, 41-52; Yohane 1:9) 
- 9:25 Nyimbo Na. 69 na Zilengezo 
- 9:35 YOSIYILANA: Maulosi Okhudza Mesiya Anakwanilitsika! - • Pambuyo pa Mthenga (Malaki 3:1; 4:5; Mateyu 11:10-14) 
- • Anabadwa kwa Namwali (Yesaya 7:14; Mateyu 1:18, 22, 23) 
- • Anabadwila ku Betelehemu (Mika 5:2; Luka 2:4-7) 
- • Anatetezedwa Ali Mwana (Hoseya 11:1; Mateyu 2:13-15) 
- • Anachedwa Mnazareti (Yesaya 11:1, 2; Mateyu 2:23) 
- • Anafika pa Nthawi Yoikika (Danieli 9:25; Luka 3:1, 2, 21, 22) 
 
- 10:40 UBATIZO: Pitilizani ‘Kugonjela Uthenga Wabwino’ (2 Akorinto 9:13; 1 Timoteyo 4:12-16; Aheberi 13:17) 
- 11:10 Nyimbo Na. 24 na Kupumula 
Masana
- 12:35 Vidiyo ya Nyimbo 
- 12:45 Nyimbo Na. 83 
- 12:50 YOSIYILANA: Seŵenzetsani Uthenga Wabwino Pogonjetsa Uthenga Woipa - • Mijedo Yovulaza (Yesaya 52:7) 
- • Cikumbumtima Covutitsidwa (1 Yohane 1:7, 9) 
- • Zinthu Zimene Zikucitika Masiku Ano (Matthew 24:14) 
- • Zolefula (Mateyu 11:28-30) 
 
- 13:35 YOSIYILANA: “Ofunitsitsa Kulengeza Uthenga Wabwino” - • Sinali Nchito ya Atumwi Okha (Aroma 1:15; 1 Atesalonika 1:8) 
- • Ni Mbali ya Kulambila (Aroma 1:9) 
- • Khalani Okonzeka Pokhala na Zida Zoyenela (Aefeso 6:15) 
 
- 14:15 VIDIYO: Mmene ‘Uthenga Wabwino Ukubalila Zipatso na Kufalikila Padziko Lonse’ (Akolose 1:6) 
- 14:40 Nyimbo Na. 35 na Zilengezo 
- 14:50 YOSIYILANA: Pitilizani Kulalikila Uthenga Wabwino - • Kulikonse Kumene Mungakhale (2 Timoteyo 4:5) 
- • Kulikonse Kumene Mulungu Angakutsogoleleni (Machitidwe 16:6-10) 
 
- 15:15 Kodi Mudzacita Ciyani “Cifukwa ca Uthenga Wabwino”? (1 Akorinto 9:23; Yesaya 6:8) 
- 15:50 Nyimbo Na. 21 na Pemphelo Lothela