NYIMBO 160
“Uthenga Wabwino”!
Yopulinta
1. “Ulemelelo kwa Ya”—
Yesu wabadwa—
Iye ni mpulumutsi wathu.
Adzamasula,
Cilengedwe conse!
(KOLASI)
Yesu wabadwa—
Tonse tikondwe—
Tiuze onse!
Yesu ni njila—
Iye n’co’nadi.
Onse adziŵe—
Iye ndiye moyo.
2. Khristu adzabweletsa.
Mtendele m’dziko.
Iye ni njila ya ku moyo.
Ufumu wake.
Ulibe mapeto.
(KOLASI)
Yesu wabadwa—
Tonse tikondwe—
Tiuze onse!
Yesu ni njila—
Iye n’co’nadi.
Onse adziŵe—
Iye ndiye moyo.
(KOLASI)
Yesu wabadwa—
Tonse tikondwe—
Tiuze onse!
Yesu ni njila—
Iye n’co’nadi.
Onse adziŵe—
Iye ndiye moyo.
(Onaninso Mat. 24:14; Yoh. 8:12; 14:6; Yes. 32:1; 61:2.)