LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp18 na. 1 tsa. 16
  • Muganiza Bwanji?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Muganiza Bwanji?
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2018
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Baibo ingakuthandizeni kukhala bwenzi la Mulungu?
  • Mulungu Akupemphani Kuti Mukhale Mnzake
    Na Imwe Mungakhale Mnzake wa Mulungu!
  • Mukhoza Kukhala Bwenzi la Yehova
    Kondwelani Na Moyo Kwamuyaya!—Maphunzilo a Baibo Okambilana Komanso Zocita
  • Miyambo 17:17—“Bwenzi Lenileni Limakukonda Nthawi Zonse”
    Kufotokoza Mavesi a m’Baibulo
  • Kodi Mulungu N’ndani?
    Zimene Baibulo Ingatiphunzitse
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2018
wp18 na. 1 tsa. 16
Mwamuna na mkazi wake apita kukayenda ndipo aŵelenga Baibo

Muganiza Bwanji?

Kodi Baibo ingakuthandizeni kukhala bwenzi la Mulungu?

ANTHU ENA AMAKHULUPILILA KUTI . . .

sangakhale mabwenzi a Mulungu cifukwa amadziona kuti ni odetsedwa komanso ocimwa. Ena amakamba kuti Mulungu satidela nkhawa. Imwe muganiza bwanji?

ZIMENE BAIBO IMAKAMBA

Mulungu “amakonda anthu owongoka mtima.” (Miyambo 3:32) Ngati timvela Mulungu, tingakhale mabwenzi ake.

MFUNDO ZINA ZIMENE BAIBO IMAKAMBA

  • Mulungu afuna kuti tikhale mabwenzi ake. —Yakobo 4:8.

  • Monga Bwenzi lathu, Mulungu ni wokonzeka kutikhululukila na kutithandiza.—Salimo 86:5.

  • Mabwenzi a Mulungu amakonda zimene iye amakonda na kudana na zimene amadana nazo. —Aroma 12:9.

Kuti mudziŵe zambili za mmene mungakhalile na umoyo wokondweletsa Mulungu, onani nkhani 12 m’buku imeneyi, Zimene Baibulo Ingatiphunzitse yofalitsidwa na Mboni za Yehova. Buku imeneyi ipezekanso pa webusaiti ya www.jw.org

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani