LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 February tsa. 3
  • Nehemiya anali woyang’anila wa citsanzo cabwino kwambili

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Nehemiya anali woyang’anila wa citsanzo cabwino kwambili
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Nehemiya Anali Kukonda Kulambila Koona
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Mpanda Wa Yerusalemu
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Mpanda wa Yerusalemu Umangidwanso
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Nehemiya Anali Kufuna Kutumikila Ena, Osati Kutumikilidwa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 February tsa. 3

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | NEHEMIYA 5–8

Nehemiya anali woyang’anila wa citsanzo cabwino kwambili

Tishiri 455 B.C.E.

8:1-18

  1. Zikuoneka kuti pa cocitikaci, Nehemiya analangiza anthu kusonkhana kuti alambile Mulungu

  2. Anthu anasangalala kwambili

  3. Amuna amene anali mitu ya mabanja, anasonkhana kuti aphunzile zimene zikanawathandiza kutsatila kwambili Cilamulo ca Mulungu

  4. Anthu anakonzekela Cikondwelelo ca Misasa

Aisiraeli akusonkhana kuti alambile Mulungu, alandile malangizo, ndi kucita Cikondwelelo ca Misasa m’mwezi wa Tishiri mu 455 B.C.E
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani