LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 May tsa. 2
  • Kodi Mukugwilitsila Nchito JW Laibulale?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mukugwilitsila Nchito JW Laibulale?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Laibulali Imene Mungathe Kuinyamula Kumanja
    Mmene Zopeleka Zanu Zimagwilila Nchito
  • Mmene Tingaseŵenzetsele JW Laibulale
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Kabokosi Kakang’ono Kopelekela Cakudya Cauzimu
    Mmene Zopeleka Zanu Zimagwilila Nchito
  • Kodi Tingapindule Bwanji ndi Laibulale ya pa Nyumba ya Ufumu?
    Ndani Amene Akucita Cifunilo Ca Yehova Masiku Ano?
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 May tsa. 2

UMOYO WATHU WACIKRISTU

Kodi Mukugwilitsila Nchito JW Laibulale?

JW Laibulale ndi pulogalamu ya pa kompyuta imene mungagwilitsile nchito potenga Baibulo, zofalitsa zina, mavidiyo, ndi zinthu zina zomvetsela ndi kuziika pa foni, pa tabuleti kapena pa kompyuta yanu.

Mabuku a m’Baibulo pa JW Library

MMENE MUNGAIKILE JW LAIBULALE PA CIPANGIZO CANU: Pitani pa intaneti ndi kuika JW Laibulale pa cipangizo canu. JW Laibulale imapezeka mu app store. Mungathe kuika JW Laibulale pa zipangizo zosiyanasiyana. Mukali pa intaneti, tsegulani JW Laibulale ndi kuika zofalitsa zimene mukufuna pa cipangizo canu. Ngati mulibe intaneti, mungapite ku Nyumba ya Ufumu ngati iliko, kapena pamalo ena alionse kumene kungapezeke intaneti. Mukaika zofalitsa pa cipangizo canu, mungazitsegule nthawi iliyonse pamene mukuzifuna ngakhale kulibe intaneti. Komabe, popeza zinthu zina zatsopano zimaikidwa pa JW Laibulale, mufunika kupita pa intaneti nthawi ndi nthawi kuti mutenge zinthu zatsopanozo.

UBWINO WA JW LAIBULALE. Pulogalamu imeneyi imathandiza pocita phunzilo laumwini ndi pamisonkhano. Imathandizanso mu ulaliki, makamaka pocita ulaliki wamwamwai.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani