CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 92-101
Amabala Zipatso Ngakhale ni Okalamba
92:12
Mitengo ina ya kanjedza imakhala zaka zoposa 100, ndipo imabalabe zipatso
Acikulile amabala zipatso zauzimu mwa . . .
92:13-15
kupemphelela ena
kuphunzila Baibulo
kupezeka pamisonkhano na kuyankhapo
kuuzako ena zinthu zimene adziŵa
kulalikila modzipeleka