CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | LUKA 2-3
Acicepele—Kodi Mukukula Mwauzimu?
Kungoyambila ali mwana, Yesu anapeleka citsanzo cabwino kwambili pa nkhani yotumikila Yehova na kulemekeza makolo ake.
Acicepele, kodi mungatengele bwanji citsanzo ca Yesu m’mbali zotsatilazi?