LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 July tsa. 5
  • Kalamilani Nchito Yabwino

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kalamilani Nchito Yabwino
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Abale Acinyamata, Kodi Mukukalamila?
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • “N’cifukwa Ciyani Akhristu Ayenela Kuyesetsa Kuwonjezela Utumiki Wawo?”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Acicepele—Kodi Mukukula Mwauzimu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Atumiki Othandiza Amacita Utumiki Wofunika
    Gulu Lokhazikitsidwa Kucita Cifunilo ca Yehova
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 July tsa. 5
M’bale wacicepele akupelekela maikolofoni pa misonkhano ya mpingo, acita phunzilo la umwini, ndipo akuyendetsa mlongo wacikulile pa njinga ya olemala

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 1 TIMOTEYO 1-3

Kalamilani Nchito Yabwino

3:1, 13

Zimakhala bwino ngati abale ayamba kukalamila ali acicepele. Izi zimawapatsa mwayi wakuti aphunzitsidwe, na kuonetsa kuti ni oyenelela kulandila udindo wokhala mtumiki wothandiza akadzakula. (1 Tim. 3:10) Kodi m’bale angacite ciani kuti akalamile udindo? Angacite zimenezi mwa kukulitsa na kuonetsa makhalidwe otsatilawa:

  • Kudzipeleka pa nchito.—km 7/13 2-3 ¶2

  • Kukonda zinthu zauzimu.—km 7/13 3 ¶3

  • Kudalilika na kukhulupilika.—km 7/13 3 ¶4

M’bale akamba na m’bale wacicepele pamene akumuphunzitsa kutumikila mu mpingo
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani