LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 January tsa. 4
  • “Inu Mulungu Wanga, Cikhulupililo Canga Cili mwa Inu”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Inu Mulungu Wanga, Cikhulupililo Canga Cili mwa Inu”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Nkhani Zofanana
  • Mulungu Athandiza Mfumu Hezekiya
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Kodi Abusa 7 Ndi Atsogoleli 8 Ndani Masiku Ano?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2013
  • N’zotheka Kuti Muziwadalila Abale Anu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2022
  • Kodi Mudzacita Ciani pa Nthawi ya Cilala?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 January tsa. 4

UMOYO WACIKHIRISTU

“Inu Mulungu Wanga, Cikhulupililo Canga Cili mwa Inu”

Hezekiya apemphela

Tifunika kudalila Yehova kwambili pamene zinthu zikuyenda bwino ndi pa nthawi yovuta. (Sal. 25:1, 2) M’zaka za m’ma 700 B.C.E., Ayuda ku Yudeya anakumana ndi vuto imene inayesa cikhulupililo cawo mwa Mulungu. Tingaphunzile zambili pa zimene zinacitika. (Aroma 15:4) Mukatamba vidiyo yakuti, “Inu Mulungu Wanga, Cikhulupililo Canga Cili mwa Inu” yankhani mafunso aya.

  1. Kodi Hezekiya anakumana ndi cothetsa nzelu canji?

  2. Kodi Hezekiya anaseŵenzetsa bwanji mfundo ya pa Miyambo 22:3 atadziŵa kuti adani akubwela kudzazinga mzinda wawo?

  3. N’cifukwa ciani Hezekiya anakanilatu zodzipeleka kwa Asuri, kapena kupanga mgwilizano ndi Aiguputo?

  4. Kodi Hezekiya ni citsanzo cabwino motani kwa Akhiristu?

  5. N’zocitika ziti zimene zingatiyese pa cidalilo cathu mwa Yehova?

N’dzadalila Yehova kwambili pa zocitika izi . . .

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani