LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 January tsa. 5
  • ezekiya Anafupidwa Cifukwa ca Cikhulupililo Cake

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • ezekiya Anafupidwa Cifukwa ca Cikhulupililo Cake
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Nkhani Zofanana
  • Mngelo wa Yehova Ateteza Hezekiya
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Mulungu Athandiza Mfumu Hezekiya
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Kodi Abusa 7 Ndi Atsogoleli 8 Ndani Masiku Ano?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2013
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 January tsa. 5

CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU | YESAYA 34-37

Hezekiya Anafupidwa Cifukwa ca Cikhulupililo Cake

 Rabisake ndi asilikali ake ali kunja kwa mpanda wa Yerusalemu

Mfumu Senakeribu ya Asuri inatuma Rabisake ku Yerusalemu kukauza Hezekiya kuti angopeleka mzindawo. Asuri anaseŵenzetsa njila zosiya-nasiyana pofuna kuwayofya Ayuda kuti adzipeleke popanda kumenyana nawo.

  • Asilikali acisuri ali kunja kwa mpanda wa Yerusalemu

    Kuwapatula. Aiguputo sangakuthandizeni konse.—Yes. 36:6

  • Anthu ni okayikila

    Kuwakaikitsa. Yehova sadzakumenyelani nkhondo cifukwa munam’khumudwitsa.—Yes. 36:7, 10

  • Asilikali acisuri

    Kuwayofya. Mwacepa kutali-tali kwa asilikali amphamvu a Asuri.—Yes. 36:8, 9

  • Malo okhala ndi munda waukulu

    Kuwanyengelela. Mukadzipeleka kwa Asuri zinthu zidzakuyendelani bwino.—Yes 36:16, 17

Hezekiya anaonetsa cikhulupililo cosagwedela mwa Yehova

37:1, 2, 14-20, 36

  • Anacita zonse zotheka kuti ateteze mzinda kwa adani odzauzinga

  • Anapemphela kwa Yehova kuti awalanditse, ndi kulimbikitsanso anthu ake kucita cimodzi-modzi

  • Yehova anamufupa mwa kutumiza mngelo amene anapha asilikali acisuri 185,000 usiku umodzi cabe

    Hezekiya apemphela ndipo mngelo agwila lupanga
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani