January Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhiristu—Kabuku ka Misonkhano January 2017 Maulaliki a Citsanzo January 2-8 CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU | YESAYA 24-28 Yehova Amasamalila Anthu Ake January 9-15 CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU | YESAYA 29-33 “Mfumu Idzalamulila Mwacilungamo” January 16-22 CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU | YESAYA 34-37 ezekiya Anafupidwa Cifukwa ca Cikhulupililo Cake UMOYO WACIKHIRISTU “Inu Mulungu Wanga, Cikhulupililo Canga Cili mwa Inu” January 23-29 CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU | YESAYA 38-42 Yehova Amapeleka Mphamvu kwa Munthu Wotopa UMOYO WACIKHIRISTU Tizikumbukila Kupemphelela Akhiristu Anzathu Amene Akuzunzidwa January 30–February 5 CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU | YESAYA 43-46 Maulosi Onse a Yehova Amakwanilitsika