January 30–February 5
YESAYA 43-46
Nyimbo 33 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Maulosi Onse a Yehova Amakwanilitsika”: (10 min.)
Yes. 44:26-28—Yehova anakambilatu kuti Yerusalemu na kacisi adzamangiwanso, ndipo anati Koresi ni amene adzagonjetsa Babulo (ip-2 71-72 pala. 22-23)
Yes. 45:1, 2—Yehova anafotokozelatu mmene mzinda wa Babulo udzagonjetsedwela (ip-2 77-78 pala. 4-6)
Yes. 45:3-6—Yehova anakamba zifukwa zimene anaseŵenzetsela Koresi kugonjetsa Babulo (ip- 2 79-80 pala. 8-10)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yes. 43:10-12—Kodi Aisiraeli anakhala bwanji mtundu wa mboni za Yehova? (w14 11/15 peji 21-22 pala. 14-16)
Yes. 43:25, Buku lopatulika—Kodi cifukwa cikulu cimene Yehova amafafanizila zolakwa zathu n’ciani? (ip-2 peji 60 pala. 24)
Kodi ine pacanga, kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno zimene ine pacanga ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. kapena zocepelapo) Yes. 46:1-13
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. kapena zocepelapo) fg—Citani ulaliki wamwamwai kwa mnzanu wa kusukulu kapena wa kunchito.
Ulendo Wobwelelako: (4 min. kapena zocepelapo) fg—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.
Phunzilo la Baibo: (6 min. kapena zocepelapo) jl phunzilo 4
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
Tingatsimikizile Bwanji Kuti Baibulo Limakamba Zoona?: (15 min.) Tambitsani Vidiyo imeneyi yakuti Tingatsimikizile Bwanji Kuti Baibulo Limakamba Zoona? (Yendani ku mavidiyo pa MISONKHANO NA UTUMIKI WATHU). Ndiyeno kambilanani mafunso aya: Kodi vidiyo imeneyi tingaiseŵenzetse bwanji polalikila mwamwai, pa ulaliki wapoyela, kapena polalikila ku nyumba na nyumba? Tisimbilen’koni zabwino zimene zinacitika potambitsa vidiyoyi mu ulaliki?
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 7 pala. 19-23, bokosi papeji 75, na chati papeji 76-77, na bokosi lobwelelamo papeji 77
Kubwelelamo na Kuchulako za Mlungu Wotsatila (3 min)
Nyimbo 103 na Pemphelo