CUMA COCOKELA M’MAU A MULUNGU | YESAYA 43-46
Maulosi Onse a Yehova Amakwanilitsika
Yopulinta
Pafupi-fupi zaka 200 Babulo akalibe kugonjetsewa, Yehova anakambilatu, kupitila mwa mneneli Yesaya, tsatane-tsatane wa zimene zidzacitika.
44:27–45:2
Koresi ndiye adzagonjetsa Babulo
Zitseko za mzindawo zidzasiiwa zotsegula
Mtsinje wa Firate umene unali kupeleka citetezo ku mzindawu udzaphwila