CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YEREMIYA 17-21
Lolani Kuti Yehova Aumbe Maganizo na Khalidwe Lanu
Lolani Kuti Yehova Akuumbeni
18:1-11
Yehova amaumba makhalidwe athu a kuuzimu mwa kutipatsa uphungu ndi kutilanga
Tifunika kukhala ofeŵa ndi omvela
Yehova satikakamiza kucita zimene sitifuna
Woumba angasinthe maganizo ake a moseŵenzetsela cimene waumba
Popeza Yehova anatipatsa ufulu wosankha zocita, tingasankhe kumulola kutiumba kapena kukana
Yehova amasintha mocitila ndi anthu malinga na mmene amalabadilila malangizo ake