LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 May tsa. 4
  • Yehova Saiŵala Cikondi Canu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Saiŵala Cikondi Canu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Nkhani Zofanana
  • Muziona Okalamba Okhulupilika Kuti ni Ofunika
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • Muziyamikila Mphamvu za Acinyamata
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • ‘Zimenezo Uziphunzitse kwa Amuna Okhulupilika’
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 May tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

Yehova Saiŵala Cikondi Canu

TAMBITSANI VIDIYO YAKUTI YEHOVA SAIŴALA CIKONDI CANU, NDI KUKAMBILANA MAFUNSO AYA:

  • Ni mavuto anji amene amabwela na ukalamba?

  • Nanga ni khalidwe labwino liti limene limabwela na ukalamba?

  • Ngati ndinu wokalamba, kodi malemba a Levitiko 19:32 na Miyambo 16:31 amakulimbikitsani bwanji?

  • Kodi Yehova amawaona bwanji atumiki ake okalamba amene sacita zambili mu utumiki?

  • N’ciani cimene Yehova amafuna kuti tizicitabe olo kuti takalamba?

  • Kodi okalamba angalimbikitse bwanji acicepele?

  • Kodi m’bale kapena mlongo wokalamba anakulimbikitsani bwanji posacedwa?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani