CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | EZEKIELI 15-17
Kodi Mumasunga Malonjezo Anu?
17:18, 19
Ni lumbilo lanji limene Mfumu Zedekiya anaphwanya?
Nanga panakhala zotulukapo zabwanji?
Kodi malonjezo komanso mapangano amene nʼnapanga ni ati?
N’ciani cimene cingatsatilepo nikaphwanya malonjezo kapena mapangano anga?