CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | EZEKIELI 28-31
Yehova Anadalitsa Mtundu Wacikunja
29:18-20
Ngati Yehova anadalitsa mtundu wacikunja cifukwa ca zimene unacita, kuli bwanji nanga kwa atumiki ake okhulupilika pa nchito yawo.
ZIMENE ABABULO ANACITA
Kuzinga mzinda wa Turo
ZOCITA ZANGA
Ni nkhondo ya kuuzimu iti imene nikumenya?
MMENE ABABULO ANAVUTIKILILAPO
Kuzinga mzinda wa Turo kunatenga zaka 13
Asilikali Acibabulo anavutika
Ababulo sanalandile malipilo alionse
ZIMENE NADZIMANA
Nadzimana zinthu zanji kuti nitumikile Yehova?
MMENE YEHOVA ANAWAPATSILA MPHOTO ABABULO
Yehova anawapatsa Iguputo monga cofunkha cawo
MMENE YEHOVA WANIDALITSILA
Kodi Yehova wanidalitsa bwanji?