CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | DANIELI 1-3
Kukhala Wokhulupilika kwa Yehova Kumabweletsa Madalitso
Nkhani ya Aheberi atatu ingatilimbikitse kukhalabe wokhulupilika kwa Yehova.
3:16-20, 26-29
Malinga na malemba otsatilawa, kodi kukhala wokhulupilika kwa Yehova kumaphatikizapo ciani?