CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | DANIELI 4-6
Kodi Mukutumikila Yehova Mosalekeza?
Pulogilamu ya zinthu zauzimu ya Danieli inaphatikizapo nthawi yopemphela. Iye sanalole ciliconse kusokoneza pulogilamu yake yauzimu, ngakhale lamulo la mfumu
6:10
Pulogilamu ya zinthu zauzimu imaphatikizapo: