Mawu Oyamba
Kodi ni madalitso otani amene Mulungu analonjeza anthu? Kodi mungawadalile Mawu ake? Nkhani zotsatila zidzafotokoza ena mwa malonjezo a Mulungu. Zidzafotokozanso cifukwa cake mungakhulupilile malonjezowo, komanso zimene mungacite kuti mulandile madalitso olonjezedwa, na kukhala wacimwemwe.