LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 April tsa. 7
  • Kuseŵenzetsa Mwaluso Zida Zophunzitsila za mu Thuboksi Yathu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kuseŵenzetsa Mwaluso Zida Zophunzitsila za mu Thuboksi Yathu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Kuphunzitsa Coonadi
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
  • Zida Zathu Zophunzitsila
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 April tsa. 7

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Kuseŵenzetsa Mwaluso Zida Zophunzitsila za mu Thuboksi Yathu

Aseŵenzetsa Baibo na kabuku polalikila munthu

Kupanga ophunzila kuli ngati kumanga nyumba. Kuti tiimange bwino nyumbayo, tifunika kudziŵa moseŵenzetsela zida zomangila. Tiyenela kukulitsa luso lathu loseŵenzetsa Mau a Mulungu, amene ndico cida cathu cacikulu. (2 Tim. 2:15) Tiyenelanso kuseŵenzetsa mwaluso zofalitsa zina na mavidiyo a mu Thuboksi yathu ya zida Zophunzitsila—tili na colinga copanga ophunzila.a

Munganole bwanji luso lanu loseŵenzetsa zida zophunzitsila za mu Thuboksi yathu? (1) Pemphani woyang’anila kagulu kanu kuti akuthandizeni, (2) lalikilani pamodzi na wofalitsa amene ni ciyambakale kapena mpainiya, ndipo (3) muziyeseza. Ngati museŵenzetsa mwaluso zofalitsa zimenezi na mavidiyo, mudzakhala acimwemwe pogwila nchito yomanga yauzimu imene ikucitika pali pano.

MAGAZINI

Nsanja ya Mlonda
Galamuka!

TUMABUKU

Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya
Ndani Amene Akucita Cifunilo ca Yehova Masiku Ano?
Uthenga Wocokela Kwa Mulungu

MABUKU

Zimene Baibulo Ingatiphunzitse
Mmene Tingakhalilebe M’cikondi ca Mulungu

TUMAPEPA TWA UTHENGA

Kodi Baibo Mumaiona Bwanji?
Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?
Kodi Cofunika N’ciani Kuti Banja Likhale Lamtendele?
Kodi Ndani Maka-maka Amene Akulamulila Dzikoli?
Kodi Mavuto Adzathadi?
Kodi N’zoona Kuti Akufa Angakhalenso ndi Moyo?
Kodi Ufumu wa Mulungu Ndi Ciani?
Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambili Onena za Umoyo?

MAVIDIYO

N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo?
Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji?
N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu?
Mboni za Yehova—Kodi Ndife Anthu Otani?

TUMAPEPA TWA CIITANILO

Kapepa Koitanila ku Misonkhano

TUMAKADI TONGENELA PA WEBUSAITI

Khadi yongenela pa Webusaiti

a Zofalitsa zocepa zimene sizipezeka mu Thuboksi yathu anazilembela magulu ena-ake a anthu. Zofalitsazi tingaziseŵenzetse pakakhala pofunikila.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani