Alalikila ku Tonga
Makambilano Acitsanzo
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Tingadziŵe bwanji zimene zidzacitika m’tsogolo?
Lemba: Yes. 46:10
Ulalo: Kodi Mulungu analonjeza kuti zinthu m’tsogolo zidzakhala bwanji kwa anthu pa dziko lapansi?
○●○ KUBWELELAKO KOYAMBA
Funso: Kodi Mulungu analonjeza kuti zinthu m’tsogolo zidzakhala bwanji kwa anthu pa dziko lapansi?
Lemba: Sal. 37:29
Ulalo: Tingacite ciani kuti tikaone kukwanilitsidwa kwa lonjezo la m’Baibo limeneli?
○○● KUBWELELAKO KACIŴILI
Funso: Tingacite ciani kuti tikaone kukwanilitsidwa kwa lonjezo la m’Baibo limeneli?
Lemba: Sal. 37:34
Ulalo: Kodi Mulungu amafuna kuti tizikhala na umoyo wabwanji?