LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 June tsa. 1
  • Makambilano Acitsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Makambilano Acitsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • ●○○ ULENDO WOYAMBA
  • ○●○ KUBWELELAKO KOYAMBA
  • ○○● KUBWELELAKO KACIŴILI
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 June tsa. 1
Makolo ku South Africa akuŵelenga ndi ana awo

Makolo ku South Africa akuphunzitsa ana awo

Makambilano Acitsanzo

●○○ ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi tingadziŵe bwanji za kutsogolo?

Lemba: Yes. 46:10

Ulalo: Ni maulosi ati a m’Baibo amene akukwanilitsidwa masiku ano?

○●○ KUBWELELAKO KOYAMBA

Funso: Ni maulosi ati a m’Baibo amene akukwanilitsidwa masiku ano?

Lemba: Mat. 24:6, 7, 14

Ulalo: N’ciani cidzacitika pambuyo pa “mapeto”?

○○● KUBWELELAKO KACIŴILI

Funso: N’ciani cidzacitika pambuyo pa “mapeto”?

Lemba: Chiv. 21:4

Ulalo: Kodi ulosi wa m’Baibo umenewu udzakwanilitsidwila kuti?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani