CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MALIKO 7-8
Nyamula Mtengo Wako Wozunzikilapo ndi Kunditsatila Mosalekeza
Yesu anakamba kuti: ‘Munditsatile mosalekeza.’ Conco, tifunika kupilila. Tingaonetse bwanji kuti tikumutsatila mosalekeza pa nkhani ya . . .
pemphelo?
kuŵelenga?
kulalikila?
kusonkhana?
kupeleka ndemanga pa misonkhano?